Mark 9:16 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Iye adaŵafunsa kuti, “Kodi mukutsutsana zotani?”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anawafunsa iwo, Mufunsana nao chiyani?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iye anafunsa kuti, “Mukukangana nawo chiyani iwowa?”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anawafunsa iwo, Mufunsa na nao ciani?