Mark 9:29 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Yesu adayankha kuti, “Mzimu wa mtundu umenewu, pokhapokha mutayamba mwapemphera mpamene mungautulutse.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Iye anati kwa iwo, Mtundu uwu sukhoza kutuluka ndi kanthu kena konse, koma ndi kupemphera.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iye anayankha kuti, “Mtundu uwu umatuluka pokhapokha mwapemphera ndi kusala kudya.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Iye anati kwa iwo, Mtundu uwu sukhoza kuturuka ndi kanthu kena konse, koma ndi kupemphera.