Mark 9:30 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Atachoka kumeneko, Yesu ndi ophunzira ake ankadutsa m'dziko la Galileya. Koma Iye sadafune kuti anthu adziŵe,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anachoka iwo kumeneko, napyola pakati pa Galileya; ndipo Iye sanafune kuti munthu adziwe.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Anachoka malo amenewo nadutsa ku Galileya. Yesu sanafune kuti wina aliyense adziwe kumene anali,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anacoka iwo kumeneko, napyola pakati pa Galileya; ndipo Iye sanafuna kuti munthu adziwe.