Matthew 1:8 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Asa adabereka Yehosafati, Yehosafati adabereka Yoramu, Yoramu adabereka Uziya.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndi Asa anabala Yehosafati; ndi Yehosafati anabala Yoramu; ndi Yoramu anabala Uziya;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Asa anabereka Yehosafati, Yehosafati anabereka Yoramu, Yoramu anabereka Uziya.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndi Asa anabala Yosafate; ndi Yosafate anabala Yoramu; ndi Yoramu anabala Uziya;