Matthew 10:6 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma makamaka mupite kwa Aisraele amene ali ngati nkhosa zotayika.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
koma makamaka mupite kunkhosa zosokera za banja la Israele.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma pitani kwa nkhosa zotayika za banja la Israeli.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
koma makamaka mupite ku nkhosa zosokera za banja la Israyeli.