Matthew 10:9 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Musatenge ndalama m'zikwama, kaya nzagolide, kaya nzasiliva, kaya nzakopala.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Musadzitengere ndalama zagolide, kapena zasiliva, kapena zakobiri m'malamba mwanu;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Musatenge ndalama zagolide kapena zasiliva kapena zakopala mʼzikwama mwanu;
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Musadzitengere ndalama zagolidi, kapena zasiliva, kapena zakobiri m'malamba mwanu;