Matthew 12:10 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
M'menemo munali munthu wopuwala dzanja. Tsono anthu ena amene ankafuna chifukwa choti akamnenezere Yesuyo, adamufunsa kuti, “Kodi Malamulo amalola kuchiritsa munthu pa tsiku la Sabata?”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndipo onani, munali munthu wa dzanja lopuwala. Ndipo anamfunsitsa Iye, ndi kuti, Nkuloleka kodi kuchiritsa tsiku la Sabata? Kuti ampalamulitse mlandu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo mʼmenemo munali munthu wolumala dzanja. Pofuna chifukwa chokamunenezera, iwo anamufunsa Yesu kuti, “Kodi nʼkololedwa kuchiritsa munthu tsiku la Sabata?”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndipo onani, munali munthu wa dzanja lopuwala, Ndipo anamfunsitsa Iye, ndi kuti, Nkuloleka kodi kuciritsa tsiku la Sabata? kuti ampalamulitse mlandu.