Matthew 12:14 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pamenepo Afarisi aja adatuluka nakachita upo kuti apangane njira yophera Yesu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Afarisi anatuluka, nakhala upo womchitira Iye mwa kumuononga.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma Afarisi anatuluka kunja ndi kukonza njira yoti amuphere.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Afarisi anaturuka, nakhala upo womcitira Iye mwa kumuononga.