Matthew 12:19 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Iye sadzachita makani, kapena kufuula. Palibe munthu wodzamva mau ake m'miseu ya m'mizinda.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Sadzalimbana, sadzafuula; ngakhale mmodzi sadzamva mau ake m'makwalala;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Sadzalimbana, sadzafuwula, ngakhale mmodzi sadzamva mawu ake mʼmakwalala.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Sadzalimbana, sadzapfuula; Ngakhale mmodzi sadzamva mau ace m'makwalala;