Matthew 12:48 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Yesu adamuyankha kuti, “Kodi ine amai anga ndani? Ndipo abale anga ndani?”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma Iye anayankha, nati kwa iye wonenayo, Amai wanga ndani, ndipo abale anga ndi ayani?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iye anayankha kuti, “Amayi anga ndani ndipo abale anga ndi ndani?”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma Iye anayankha, nati kwa iye wonenayo, Amai wanga ndani? ndi abale anga ndi ayani?