Matthew 12:6 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndipotu ndikunenetsa kuti pali wina pano woposa Nyumba ya Mulunguyo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma ndinena kwa inu, kuti wakuposa Kachisiyo ali pompano.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ine ndikuwuzani kuti wamkulu kuposa Nyumba ya Mulunguyo ali pano.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma ndinena kwa inu, kuti wakuposa Kacisiyo ali pompano.