Matthew 12:7 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mukadadziŵa tanthauzo la mau a Mulungu aja akuti, ‘Ndimafuna chifundo, osati nsembe ai,’ sibwenzi mutaweruza kuti ndi olakwa anthu amene sadalakwe konse.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma mukadadziwa nchiyani ichi, Ndifuna chifundo, si nsembe ai; simukadaweruza olakwa iwo osachimwa,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ngati mukanadziwa zomwe mawu awa atanthauza, ‘Ine ndifuna chifundo osati nsembe,’ inu simukanatsutsa osalakwa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma mukadadziwa nciani ici: Ndifuna cifundo, si nsembe ai; simukadaweruza olakwa iwo osacimwa,