Matthew 12:8 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pajatu Mwana wa Munthu ali ndi ulamuliro wonse pa zokhudza tsiku la Sabata.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
pakuti Mwana wa Munthu ali mwini tsiku la Sabata.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pakuti Mwana wa Munthu ndiye Mbuye wa Sabata.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
pakuti Mwana wa munthu ali mwini tsiku la Sabata.