Matthew 13:16 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Koma inu ndinu odala, popeza kuti maso anu akupenya, ndipo makutu anu akumva.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma maso anu ali odala, chifukwa apenya; ndi makutu anu chifukwa amva.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma maso anu ndi odala chifukwa amapenya ndi makutu anu chifukwa amamva.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma maso anu ali odala, cifukwa apenya; ndi makutu anu cifukwa amva.