Matthew 13:29 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma iye adati, ‘Iyai, mungakazulire kumodzi ndi tirigu pozula namsongoleyo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma iye anati, Iai, kuti kapena m'mene mukasonkhanitsa namsongoleyo, mungazulenso tirigu pamodzi naye.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Iye anakana nati, ‘Ayi. Chifukwa pamene mukuzula namsongoleyo mwina inu mungazulire pamodzi ndi tirigu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma iye anati, lai, kuti kapena m'mene mukasonkhanitsa namsongoleyo, mungazulenso tirigu pamodzi naye.