Matthew 13:35 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Zidaatero kuti zipherezere zimene mneneri adaanena kuti, “Ndidzalankhula nawo m'mafanizo. Ndidzaulula zimene zinali zobisika chilengedwere dziko lapansi.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
kuti chikachitidwe chonenedwa ndi mneneri, kuti, Ndidzatsegula pakamwa panga ndi mafanizo; ndidzawulula zinthu zobisika chiyambire kukhazikidwa kwake kwa dziko lapansi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kotero zinakwaniritsidwa zimene zinayankhulidwa ndi mneneri kuti, “Ndidzatsekula pakamwa panga ndi mafanizo, ndidzawulula zinthu zobisika chiyambire kukhazikidwa kwa dziko lapansi.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
kuti cikacitidwe conenedwa ndi mneneri, kuti, Ndidzatsegula pakamwa panga ndi mafanizo; Ndidzaulula zinthu zobisika ciyambire kukhazikidwa kwace kwa dziko lapansi.