Matthew 13:37 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Yesu adati, “Wofesa mbeu zabwino uja ndi Mwana wa Munthu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Iye anayankha nati, Wofesa mbeu yabwino ndiye Mwana wa Munthu;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iye anayankha nati, “Munthu amene anafesa mbewu yabwino ndi Mwana wa Munthu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Iye anayankha nati, Wofesa mbeu yabwino ndiye Mwana wa munthu;