Matthew 13:47 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Ufumu wakumwamba ulinso ngati khoka limene anthu amaliponya m'nyanja, ndipo limagwira nsomba za mitundu yonse.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndiponso, Ufumu wa Kumwamba uli wofanana ndi khoka loponyedwa m'nyanja, ndi kusonkhanitsa pamodzi za mitundu yonse;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Komanso Ufumu wakumwamba ufanana ndi khoka limene linaponyedwa mʼnyanja ndipo linakola mitundu yonse ya nsomba.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndiponso, Ufumu wa Kumwamba uli wofanana ndi khoka loponyedwa m'nyanja, ndi 1 kusonkhanitsa pamodzi za mitundu yonse;