Matthew 13:56 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kodi suja alongo ake onse ali nafe pompano? Nanga tsono zonsezi adazitenga kuti?”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo alongo ake sali ndife onsewa? Ndipo Iyeyo adazitenga zinthu zonsezi kuti?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kodi alongo ake onse sali ndi ife? Tsono ndi kuti kumene anazitenga zinthu izi?”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo alongo ace sali ndife onsewa? Ndipo iyeyo adazitenga zinthu zonsezi kuti?