Matthew 13:7 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mbeu zina zidagwera pa zitsamba zaminga. Zitsambazo pokula zidalanda chakudya cha mbeu zija.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma zina zinagwa paminga, ndipo mingayo inayanga, nizitsamwitsa izo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mbewu zina zinagwa pa minga ndipo mingayo inayanga ndi kuzirepheretsa kukula.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma zina zinagwa paminga, ndipo mingayo inayanga, nizitsamwitsa izo.