Matthew 14:11 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mutuwo adautengera m'mbale nakaupereka kwa mtsikana uja, mtsikanayo nkukaupereka kwa mai wake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anautenga mutu wake m'mbalemo, naupatsa buthulo: ndipo iye anamuka nao kwa amake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mutu wake anawubweretsa mʼmbale ndi kumupatsa mtsikanayo amene anawutengera kwa amayi ake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anautenga mutu wace m'mbizimo, naupatsa buthulo: ndipo iye anamuka nao kwa amace.