Matthew 14:2 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono adauza nduna zake kuti, “Ameneyu ndi Yohane Mbatizi uja, adauka kwa akufa, nkuwona akuchita zamphamvu zonsezi.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
nanena kwa anyamata ake, Uyo ndiye Yohane Mbatizi; anauka kwa akufa; ndipo chifukwa cha ichi zamphamvuzi zilimbalimba mwa iye.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo iye anati kwa antchito ake, “Uyu ndi Yohane Mʼbatizi; iye wauka kwa akufa! Ichi ndi chifukwa chake mphamvu zodabwitsa zikugwira ntchito mwa iye.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
nanena kwa anyamata ace, U yo ndiye Yohane Mbatizi; anauka kwa akufa; ndipo cifukwa ca ici zamphamvuzi zilimbalimba mwa iye.