Matthew 14:25 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
M'mamaŵa kukali mbuu, Yesu adadza kwa iwo Iye akuyenda pa madzi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo pa ulonda wachinai wa usiku, Iye anadza kwa iwo, nayenda pamwamba pa nyanja.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pa ora lachinayi usiku, Yesu anabwera kwa iwo akuyendabe pa nyanja.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo pa ulonda wacinai wa usiku, Iye anadza kwa iwo, nayenda pamwamba pa nyanja.