Matthew 14:6 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pa tsiku lokumbukira kubadwa kwa Herode, mwana wamkazi wa Herodiasi adaavina pamaso pa anthu oitanidwa ku phwando, mwakuti adaakondwetsa Herode kwambiri.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma pakufika tsiku la kubadwa kwake kwa Herode, mwana wamkazi wa Herodiasi anavina pakati pao, namkondweretsa Herode.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pa tsiku lokumbukira kubadwa kwa Herode, mwana wamkazi wa Herodia anavina pamaso pa anthu ndipo anasangalatsa kwambiri.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma pakufika tsiku la kubadwa kwace kwa Herode, mwana wamkazi wa Herodiya anabvina pakati pao, namkondweretsa Herode.