Matthew 15:12 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pamenepo ophunzira ake adadzamufunsa kuti, “Kodi mukudziŵa kuti Afarisi aja akhumudwa atamva zija mwanenazi?”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pomwepo anadza ophunzira, nanena kwa Iye, Mudziwa kodi kuti Afarisi anakhumudwa pakumva chonenacho?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pamenepo ophunzira anabwera kwa Iye ndipo anamufunsa kuti, “Kodi mukudziwa kuti Afarisi anakhumudwa pamene anamva mawu aja?”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pomwepo anadza ophunzira, nanena kwa Iye, Mudziwa kodi kuti Afarisi anakhumudwa pakumva conenaco?