Matthew 15:2 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Chifukwa chiyani ophunzira anu sasunga mwambo wa makolo? Sasamba m'manja moyenera akamadya chakudya.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ophunzira anu alumphiranji miyambo ya makolo? Pakuti sasamba manja pakudya.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Chifukwa chiyani ophunzira anu amaphwanya mwambo wa akuluakulu? Iwo sasamba mʼmanja pakudya!”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ophunzira anu alumphiranji miyambo ya makolo? pakuti sasamba manja pakudya.