Matthew 15:20 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Zimenezi ndizo zimaipitsa munthu. Koma kudya chakudya osasamba m'manja, sikungaipitse munthu.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
izi ndizo ziipitsa munthu, koma kudya osasamba manja sikuipitsa munthu ai.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Izi ndi zimene zimachititsa munthu kukhala woyipa; koma kudya ndi mʼmanja mosasamba sikumuchititsa munthu kukhala woyipa.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
izi ndizo ziipitsa munthu, koma kudya osasamba manja sikuipitsa munthuai.