Matthew 15:26 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Yesu adamuuza kuti, “Sibwino kutenga chakudya cha ana nkuponyera agalu.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Iye anayankha, nati, Sichabwino kutenga mkate wa ana, ndi kuuponyera tiagalu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iye anayankha kuti, “Sibwino kutenga chakudya cha ana ndi kuponyera agalu.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Iye anayankha, nati, Sicabwino kutenga mkate wa ana, ndi kuuponyera tiagaru.