Matthew 15:33 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ophunzirawo adamufunsa kuti, “Anthu ochuluka chotereŵa tingaŵapezere kuti chakudya chokwanira, kuthengo ngati kuno?”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo ophunzira ananena kwa Iye, Tiione kuti mikate yotere m'chipululu yakukhutitsa unyinji wotere wa anthu?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ophunzira anayankha kuti, “Ndikuti kumene tingakapeze buledi mʼtchire muno okwanira kudyetsa gulu lotere?”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo ophunzira ananena kwa Iye, Tiione kuti mikate yotere m'cipululu yakukhutitsa unyinji wotere wa anthu?