Matthew 15:39 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pambuyo pake Yesu adatsazikana nawo anthu aja, kenaka Iye adaloŵa m'chombo napita ku dera la Magadani.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo m'mene Iye anauza makamuwo amuke, analowa m'ngalawa, nafika m'malire a Magadani.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Yesu atatha kuwuza gululo kuti lipite kwawo, analowa mʼbwato ndipo anapita kudera la Magadala.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo m'mene Iye anauza makamuwo amuke, analowa m'ngalawa, nafika m'malire Magadani.