Matthew 15:7 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Inu anthu achiphamaso, ndithu mneneri Yesaya adaanenadi zoona muja adaati,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Onyenga inu! Yesaya ananenera bwino za inu, ndi kuti,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Inu anthu achiphamaso, Yesaya ananenera za inu kuti,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Onyenga inu! Yesaya ananenera bwino za inu, ndikuti,