Matthew 16:10 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Sujanso ndi buledi msanu ndi muŵiri ndidadyetsa anthu zikwi zinai? Nanga mudaadzaza madengu angati a zotsala?
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Penanso mikate isanu ndi iwiri ija ya anthu zikwi zinai, ndi madengu angati munawatola?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kapena buledi musanu ndi muwiri amene anadya anthu 4,000, nanga ndi madengu angati amene munadzaza?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Penanso mikate isanu ndi iwiri ija ya anthu zikwi zinai, ndi malicero angati munawatola?