Matthew 16:12 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pamenepo iwo adazindikira kuti Yesu sankaŵauza kuti achenjere ndi chofufumitsira buledi, koma kuti achenjere ndi zophunzitsa za Afarisi ndi Asaduki.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pomwepo anadziwitsa kuti sanawauze kupeza chotupitsa cha mikate, koma chiphunzitso cha Afarisi ndi Asaduki.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kenaka iwo anazindikira kuti Iye samawawuza kuti achenjere ndi yisiti wa buledi koma ndi chiphunzitso cha Afarisi ndi Asaduki.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pomwepo anadziwitsa kuti sanawauza kupewa cotupitsa ca mikate, koma ciphunzitso ca Afarisi ndi Asaduki.