Matthew 16:5 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pamene ophunzira aja adakafika kutsidya, anali ataiŵala kutenga buledi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo ophunzira anadza kutsidya linalo, naiwala kutenga mikate.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma atawoloka nyanja, ophunzira anayiwala kutenga buledi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo ophunzira anadza ku tsidya linalo, naiwala kutenga mikate.