Matthew 16:7 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Apo ophunzirawo adayamba kukambirana nkumati, “Akuterotu chifukwa sitidatenge buledi.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo iwo anafunsana wina ndi mnzake, nati, Sitinatenga mikate.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iwo anakambirana pakati pawo za izi ndipo anati, “Ichi nʼchifukwa chakuti sitinatenge buledi aliyense.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo iwo anafunsana wina ndi mnzace, nati, Sitinatenga mikate.