Matthew 17:12 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma ndikunenetsa kuti Eliya adabwera kale, ndipo anthu sadamzindikire, koma adamchita zonse zimene iwo ankafuna. Chonchonso Mwana wa Munthu adzazunzidwa ndi anthuwo.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
koma ndinena kwa inu, kuti Eliya anadza kale, ndipo iwo sanamdziwe iye, koma anamchitira zonse zimene anazifuna iwo. Ndipo chonchonso Mwana wa Munthu adzazunzidwa ndi iwo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma Ine ndikuwuzani inu kuti Eliya anabwera kale koma iwo sanamuzindikire ndipo anachita naye chilichonse chimene anafuna. Momwemonso iwo adzazunza Mwana wa Munthu.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
koma ndinena kwa inu, kuti Eliya anadza kale, ndipo iwo sanamdziwa iye, koma anamcitira zonse zimene anazifuna iwo. Ndipo conconso Mwana wa munthu adzazunzidwa ndi iwo.