Matthew 17:16 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndinabwera naye kwa ophunzira anuŵa, koma alephera kumchiritsa.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo ndinadza naye kwa ophunzira anu, koma iwo sanathe kumchiritsa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ine ndinabwera naye kwa ophunzira anu koma alephera kumuchiritsa.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo ndinadza naye kwa ophunzira anu, koma iwo sanathe kumciritsa.