Matthew 17:6 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ophunzira aja atamva zimenezi, adachita mantha kwambiri nadzigwetsa chafufumimba.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo pamene ophunzira anamva, anagwa nkhope zao pansi, naopa kwakukulu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ophunzira atamva zimenezi, anachita mantha nagwa pansi chafufumimba.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo pamene ophunzira anamva, anagwa nkhope zao pansi, naopa kwakukuru.