Matthew 18:14 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chonchonso Atate anu amene ali Kumwamba safuna kuti ndi mmodzi yemwe mwa anaŵa atayike.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chomwecho sichili chifuniro cha Atate wanu wa Kumwamba kuti mmodzi wa ang'ono awa atayike.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Chimodzimodzinso Atate anu akumwamba safuna kuti mmodzi wa anawa atayike.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Comweco siciri cifuniro ca Atate wanu wa Kumwamba kuti mmodzi wa ang'ono awa atayike.