Matthew 18:35 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Inunsotu Atate anga akumwamba adzakuchitani zomwezo, aliyense mwa inu akapanda kukhululukira mbale wake ndi mtima wonse.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chomwechonso Atate wanga a Kumwamba adzachitira inu, ngati inu simukhululukira yense mbale wake ndi mitima yanu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Umu ndi mmene Atate anga akumwamba adzachitira ndi aliyense wa inu ngati simukhululukira mʼbale wanu ndi mtima wonse.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Comweconso Atate wanga adzacitira inu, ngati inu simukhululukira yense mbale wace ndi mitima yanu.