Matthew 19:20 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Munthu uja adati, “Malamulo onseŵa ndakhala ndikuŵatsata, nanga chanditsaliranso nchiyani?”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mnyamatayo ananena kwa Iye, Zonsezi ndinazisunga, ndisowanso chiyani?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mnyamatayo anati, “Zonsezi ndimazisunga, nanga chatsala ndi chiyani?”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mnyamatayo ananena kwa Iye, Zonsezi ndinazisunga, ndisowanso ciani?