Matthew 19:7 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Afarisi aja adamufunsa kuti, “Nanga bwanji Mose adalamula kuti mwamuna azipatsa mkazi wake kalata ya chisudzulo kenaka nkumuchotsa?”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Iwo ananena kwa Iye, Nanga chifukwa ninji Mose analamula kupatsa kalata wa chilekaniro, ndi kumchotsa?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo iwo anamufunsa nati, “Nanga nʼchifukwa chiyani Mose analamula kuti mwamuna azipatsa mkazi wake kalata ya chisudzulo ndi kumuchotsa?”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Iwo ananena kwa Iye, Nanga cifukwa ninji Mose analamulira kupatsa kalata wa cilekaniro, ndi kumcotsa?