Matthew 2:10 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ataiwona nyenyeziyo, adasangalala kwabasi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo iwo poona nyenyeziyo, anakondwera ndi kukondwera kwakukulu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pamene iwo anaona nyenyeziyo, anasangalala kwambiri.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo iwo poona nyenyeziyo, anakondwera ndi kukondwera kwakukuru.