Matthew 2:18 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Mau akumveka ku Rama, kulira ndi kubuma kwambiri: Rakele akulira ana ake. Akukana kumtonthoza, chifukwa ana ake asoŵa.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mau anamveka m'Rama, maliro ndi kuchema kwambiri; Rakele wolira ana ake, wosafuna kusangalatsidwa, chifukwa palibe iwo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Kulira kukumveka ku Rama, kubuma ndi kulira kwakukulu, Rakele akulirira ana ake; sakutonthozeka, chifukwa ana akewo palibe.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mau anamveka m'Rama, Maliro ndi kucema kwambiri; Rakele wolira ana ace, Wosafuna kusangalatsidwa, Cifukwa palibe iwo.