Matthew 2:20 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adamuuza kuti, “Nyamuka, tenga mwanayu ndi mai wake, ubwerere ku Israele. Aja ankafuna kumupha mwanayu adafa.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
nati, Tauka, nutenge kamwana ndi amake, nupite kudziko la Israele: chifukwa anafa uja wofuna moyo wake wa kamwanako.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
nanena kuti, “Nyamuka, tenga mwanayo ndi amayi ake ndipo mupite ku dziko la Israeli, popeza amene anafuna moyo wa mwanayo anamwalira.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
nati, Tauka, nutenge kamwana ndi amace, nupite ku dziko la Israyeli: cifukwa anafa uja wofuna moyo wace wa kamwanako.