Matthew 2:21 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Apo Yosefe adanyamuka, nkutenga mwana uja ndi mai wake, kubwerera ku Israele.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anauka iye, natenga kamwana ndi amake, nalowa m'dziko la Israele.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Tsono Yosefe atadzuka anatenga mwanayo ndi amayi ake kupita ku dziko la Israeli.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anauka iye, natenga kamwana ndi amace, nalowa m'dziko la Israyeli.