Matthew 20:29 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pamene Yesu ndi ophunzira ake ankatuluka mu mzinda wa Yeriko, anthu ambirimbiri ankamutsatira.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo pamene iwo analikutuluka m'Yeriko, khamu lalikulu la anthu linamtsata Iye.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pamene Yesu ndi ophunzira ake ankachoka ku Yeriko, gulu lalikulu la anthu linawatsata.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo pamene iwo analikuturuka m'Yeriko, khamu lalikuru la anthu linamtsata Iye.