Matthew 20:3 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pa nthaŵi ya 9 koloko adapitanso, nakapeza ena atangokhala khale pa msika, osagwira ntchito.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anatuluka dzuwa litakwera, naona ena ataima chabe pabwalo;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Nthawi 9 koloko mmawa, anatulukanso naona ena atayimirira pa msika akungokhala.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anaturuka dzuwa litakwera, naona ena ataima cabe pabwalo;