Matthew 20:7 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Iwowo adayankha kuti, ‘Chifukwa palibe amene watilemba.’ Iye uja adaŵauza kuti, ‘Inunso pitani ku munda wanga wamphesa.’
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Iwo ananena kwa iye, Chifukwa palibe munthu anatilemba. Iye anati kwa iwo, Pitani inunso kumundawo wampesa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Iwo anayankha kuti, ‘Chifukwa palibe munthu amene watilemba ganyu.’ “Iye anawawuza kuti, ‘Inunso pitani mukagwire ntchito mʼmunda wanga wa mpesa.’
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Iwo ananena kwa iye, Cifukwa palibe munthu anatilemba. Iye anati kwa iwo, Pitani inunso ku mundawo wampesa.