Matthew 21:10 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pamene Yesu adaloŵa mu Yerusalemu, mzinda wonse udatekeseka, ena nkumafunsa kuti, “Kodi ameneyu ndani?”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo m'mene adalowa m'Yerusalemu mudzi wonse unasokonezeka, nanena, Ndani uyu?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Yesu atalowa mu Yerusalemu, mzinda wonse unatekeseka ndipo anthu anafunsa kuti, “Ndani ameneyu?”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo m'mene adalowa m'Yerusalemu mudzi wonse unasokonezeka, nanena, ndani uyu?